Ekisodo 12:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndipo khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana+ anapita limodzi ndi ana a Isiraeli. Anapitanso ndi nkhosa, mbuzi ndi ng’ombe zambirimbiri. Numeri 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana+ lomwe linali pakati pawo linasonyeza mtima wadyera,+ ndipo ana a Isiraeli nawonso anayamba kulira n’kumanena kuti: “Ndani atipatse nyama yoti tidye?+
38 Ndipo khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana+ anapita limodzi ndi ana a Isiraeli. Anapitanso ndi nkhosa, mbuzi ndi ng’ombe zambirimbiri.
4 Tsopano khamu la anthu a mitundu yosiyanasiyana+ lomwe linali pakati pawo linasonyeza mtima wadyera,+ ndipo ana a Isiraeli nawonso anayamba kulira n’kumanena kuti: “Ndani atipatse nyama yoti tidye?+