Deuteronomo 1:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 komanso m’chipululu,+ kumene munaona mmene Yehova Mulungu wanu anakunyamulirani.+ M’njira yonse imene munayenda anakunyamulani ngati mmene bambo amanyamulira mwana wake, mpaka kufika malo ano.’+
31 komanso m’chipululu,+ kumene munaona mmene Yehova Mulungu wanu anakunyamulirani.+ M’njira yonse imene munayenda anakunyamulani ngati mmene bambo amanyamulira mwana wake, mpaka kufika malo ano.’+