Genesis 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ukhale ngati mlendo m’dzikoli,+ ndipo ndidzapitiriza kukhala nawe ndi kukudalitsa, chifukwa mayiko onsewa ndidzawapereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako.+ Ndidzakwaniritsa lumbiro limene ndinalumbirira Abulahamu bambo ako.+
3 Ukhale ngati mlendo m’dzikoli,+ ndipo ndidzapitiriza kukhala nawe ndi kukudalitsa, chifukwa mayiko onsewa ndidzawapereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako.+ Ndidzakwaniritsa lumbiro limene ndinalumbirira Abulahamu bambo ako.+