Genesis 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndapalana ubwenzi ndi Abulahamu kuti aphunzitse ana ake ndi mbadwa zake kuyenda m’njira ya Yehova ndi kuchita chilungamo.+ Awaphunzitse kutero, kuti Yehova adzakwaniritse kwa Abulahamu zimene ananena zokhudza iye.”+ Deuteronomo 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ndi kuwakhomereza mwa ana ako.+ Uzilankhula nawo za mawuwo ukakhala pansi m’nyumba mwako, poyenda pamsewu, pogona+ ndi podzuka. Salimo 78:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulungu anaika chikumbutso pakati pa ana a Yakobo,+Iye anaika chilamulo mu Isiraeli,+Zinthu zimene analamula makolo athu,+Kuti auze ana awo.+
19 Ndapalana ubwenzi ndi Abulahamu kuti aphunzitse ana ake ndi mbadwa zake kuyenda m’njira ya Yehova ndi kuchita chilungamo.+ Awaphunzitse kutero, kuti Yehova adzakwaniritse kwa Abulahamu zimene ananena zokhudza iye.”+
7 ndi kuwakhomereza mwa ana ako.+ Uzilankhula nawo za mawuwo ukakhala pansi m’nyumba mwako, poyenda pamsewu, pogona+ ndi podzuka.
5 Mulungu anaika chikumbutso pakati pa ana a Yakobo,+Iye anaika chilamulo mu Isiraeli,+Zinthu zimene analamula makolo athu,+Kuti auze ana awo.+