Deuteronomo 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Tsopano Aisiraeli inu, kodi Yehova Mulungu wanu akufuna kuti muzichita chiyani,+ koposa kuopa+ Yehova Mulungu wanu kuti muziyenda m’njira zake zonse,+ kukonda+ ndi kutumikira Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse,+ Deuteronomo 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Muzitsatira Yehova Mulungu wanu, muzimuopa, muzisunga malamulo ake, muzimvera mawu ake, muzim’tumikira ndi kum’mamatira.+ Salimo 34:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Opani Yehova, inu oyera ake,+Pakuti onse omuopa sasowa kanthu.+ Salimo 128:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 128 Wodala ndi aliyense woopa Yehova,+Amene amayenda m’njira za Mulungu.+
12 “Tsopano Aisiraeli inu, kodi Yehova Mulungu wanu akufuna kuti muzichita chiyani,+ koposa kuopa+ Yehova Mulungu wanu kuti muziyenda m’njira zake zonse,+ kukonda+ ndi kutumikira Yehova Mulungu wanu ndi mtima wanu wonse, ndi moyo wanu wonse,+
4 Muzitsatira Yehova Mulungu wanu, muzimuopa, muzisunga malamulo ake, muzimvera mawu ake, muzim’tumikira ndi kum’mamatira.+