Ekisodo 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo ndidzatumiza mngelo patsogolo panu+ kuti akathamangitse Akanani, Aamori, Ahiti, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+ Yoswa 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atafika, Yoswa anati: “Mukaona zimene zichitike pano, mudziwa kuti Mulungu wamoyo alidi pakati panu.+ Mudziwanso kuti iye adzathamangitsadi pamaso panu Akanani, Ahiti, Ahivi, Aperezi, Agirigasi, Aamori ndi Ayebusi.+
2 Ndipo ndidzatumiza mngelo patsogolo panu+ kuti akathamangitse Akanani, Aamori, Ahiti, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+
10 Atafika, Yoswa anati: “Mukaona zimene zichitike pano, mudziwa kuti Mulungu wamoyo alidi pakati panu.+ Mudziwanso kuti iye adzathamangitsadi pamaso panu Akanani, Ahiti, Ahivi, Aperezi, Agirigasi, Aamori ndi Ayebusi.+