Ekisodo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ Salimo 135:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ya wadzisankhira Yakobo,+Wadzisankhira Isiraeli kukhala chuma chake chapadera.+ Amosi 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ‘Pa mabanja onse apadziko lapansi+ ine ndimadziwa inu nokha.+ Choncho ndidzakulangani chifukwa cha zolakwa zanu zonse.+ Malaki 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Iwo adzakhala anthu anga,+ pa tsiku limene ndidzawasandutse chuma chapadera,”+ watero Yehova wa makamu. “Ndidzawachitira chifundo monga mmene munthu amachitira chifundo mwana wake amene amamutumikira.+
5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+
2 ‘Pa mabanja onse apadziko lapansi+ ine ndimadziwa inu nokha.+ Choncho ndidzakulangani chifukwa cha zolakwa zanu zonse.+
17 “Iwo adzakhala anthu anga,+ pa tsiku limene ndidzawasandutse chuma chapadera,”+ watero Yehova wa makamu. “Ndidzawachitira chifundo monga mmene munthu amachitira chifundo mwana wake amene amamutumikira.+