Deuteronomo 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Muziopa Yehova Mulungu wanu.+ Muzim’tumikira,+ kum’mamatira+ ndi kulumbira pa dzina lake.+ Deuteronomo 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Muzitsatira Yehova Mulungu wanu, muzimuopa, muzisunga malamulo ake, muzimvera mawu ake, muzim’tumikira ndi kum’mamatira.+
4 Muzitsatira Yehova Mulungu wanu, muzimuopa, muzisunga malamulo ake, muzimvera mawu ake, muzim’tumikira ndi kum’mamatira.+