Yoswa 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mafukowa anatenganso dziko lonse limene linali kulamulidwa ndi Ogi+ mfumu ya Basana, imene inali kulamulira ku Asitaroti ndi ku Edirei.+ Mfumu Ogi anali mmodzi mwa Arefai otsala.+ Mose anagonjetsa anthu onsewa ndi kuwapitikitsa.+
12 Mafukowa anatenganso dziko lonse limene linali kulamulidwa ndi Ogi+ mfumu ya Basana, imene inali kulamulira ku Asitaroti ndi ku Edirei.+ Mfumu Ogi anali mmodzi mwa Arefai otsala.+ Mose anagonjetsa anthu onsewa ndi kuwapitikitsa.+