Yoswa 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano Yoswa anali atakalamba, ndipo anali ndi zaka zambiri.+ Choncho Yehova anamuuza kuti: “Iweyo wakalamba ndipo uli ndi zaka zambiri, koma dziko loti lilandidwe likadali lalikulu.+
13 Tsopano Yoswa anali atakalamba, ndipo anali ndi zaka zambiri.+ Choncho Yehova anamuuza kuti: “Iweyo wakalamba ndipo uli ndi zaka zambiri, koma dziko loti lilandidwe likadali lalikulu.+