Ekisodo 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Iwe usanafike, ndidzachititsa anthu kumva za ine+ ndipo adzanjenjemera. Ndidzasokoneza anthu onse amene udzawapeze. Adani ako onse adzachita mantha ndipo adzathawa.*+ Deuteronomo 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Amuna inu, musawaope amenewo, chifukwa Yehova Mulungu wanu ndiye akukumenyerani nkhondo.’+ Deuteronomo 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyenda limodzi nanu kuti akumenyereni nkhondo ndi kukupulumutsani kwa adani anu.’+ Aroma 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+
27 “Iwe usanafike, ndidzachititsa anthu kumva za ine+ ndipo adzanjenjemera. Ndidzasokoneza anthu onse amene udzawapeze. Adani ako onse adzachita mantha ndipo adzathawa.*+
4 chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyenda limodzi nanu kuti akumenyereni nkhondo ndi kukupulumutsani kwa adani anu.’+
31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+