Yoswa 21:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Palibe lonjezo ngakhale limodzi limene silinakwaniritsidwe, pa malonjezo onse abwino amene Yehova analonjeza nyumba ya Isiraeli. Onse anakwaniritsidwa.+ 1 Mafumu 8:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 “Adalitsike Yehova+ amene wapatsa anthu ake Aisiraeli malo ampumulo, monga mwa zonse zimene analonjeza.+ Palibe mawu ndi amodzi omwe+ amene sanakwaniritsidwe pa malonjezo ake onse abwino amene analonjeza kudzera mwa Mose mtumiki wake.+
45 Palibe lonjezo ngakhale limodzi limene silinakwaniritsidwe, pa malonjezo onse abwino amene Yehova analonjeza nyumba ya Isiraeli. Onse anakwaniritsidwa.+
56 “Adalitsike Yehova+ amene wapatsa anthu ake Aisiraeli malo ampumulo, monga mwa zonse zimene analonjeza.+ Palibe mawu ndi amodzi omwe+ amene sanakwaniritsidwe pa malonjezo ake onse abwino amene analonjeza kudzera mwa Mose mtumiki wake.+