1 Samueli 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno Davide anachoka kumeneko ndi kukakhala m’malo ovuta kufikako a ku Eni-gedi.+ 2 Mbiri 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho anthu anapita kukamuuza Yehosafati kuti: “Kwabwera khamu lalikulu la anthu ochokera kuchigawo cha kunyanja,* ku Edomu,+ kudzamenyana nanu. Panopa iwo ali ku Hazazoni-tamara, kapena kuti ku Eni-gedi.”+
2 Choncho anthu anapita kukamuuza Yehosafati kuti: “Kwabwera khamu lalikulu la anthu ochokera kuchigawo cha kunyanja,* ku Edomu,+ kudzamenyana nanu. Panopa iwo ali ku Hazazoni-tamara, kapena kuti ku Eni-gedi.”+