Yoswa 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zimene zichitike n’zakuti, mapazi a ansembe onyamula likasa la Yehova, Ambuye wa dziko lonse lapansi, akangoponda m’madzi, madzi a mtsinje wa Yorodanowo aduka. Madzi otsika kuchokera kumtunda aima n’kukhala damu limodzi.”+
13 Zimene zichitike n’zakuti, mapazi a ansembe onyamula likasa la Yehova, Ambuye wa dziko lonse lapansi, akangoponda m’madzi, madzi a mtsinje wa Yorodanowo aduka. Madzi otsika kuchokera kumtunda aima n’kukhala damu limodzi.”+