Salimo 66:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anasandutsa nyanja kukhala malo ouma,+Anthu anawoloka mtsinje mwa kuyenda ndi mapazi awo.+Pamenepo tinayamba kusangalala mwa iye.+
6 Anasandutsa nyanja kukhala malo ouma,+Anthu anawoloka mtsinje mwa kuyenda ndi mapazi awo.+Pamenepo tinayamba kusangalala mwa iye.+