Yoswa 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Aliyense amene anali mumzindawo anamupha ndi lupanga, kuyambira amuna, akazi, anyamata ndi nkhalamba zomwe. Anaphanso ng’ombe, nkhosa, ndi abulu.+ Yoswa 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atatero, anatentha ndi moto mzindawo ndi zonse zimene zinali mmenemo.+ Koma siliva, golide, zipangizo zamkuwa ndi zachitsulo, anazipereka kuti zipite ku chuma cha nyumba ya Yehova.+
21 Aliyense amene anali mumzindawo anamupha ndi lupanga, kuyambira amuna, akazi, anyamata ndi nkhalamba zomwe. Anaphanso ng’ombe, nkhosa, ndi abulu.+
24 Atatero, anatentha ndi moto mzindawo ndi zonse zimene zinali mmenemo.+ Koma siliva, golide, zipangizo zamkuwa ndi zachitsulo, anazipereka kuti zipite ku chuma cha nyumba ya Yehova.+