Yoswa 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma anthu inu, mukagawe dzikolo m’zigawo 7 ndipo mukazilembe. Mukakatero, mukabwere nazo kuno kwa ine kuti ndidzakuchitireni maere+ pamaso pa Yehova Mulungu wathu.
6 Koma anthu inu, mukagawe dzikolo m’zigawo 7 ndipo mukazilembe. Mukakatero, mukabwere nazo kuno kwa ine kuti ndidzakuchitireni maere+ pamaso pa Yehova Mulungu wathu.