Oweruza 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno ana a Isiraeli anapita ku Beteli ndipo analira+ pamaso pa Yehova mpaka madzulo. Iwo anafunsira kwa Yehova, kuti: “Kodi ndipitenso kukamenyana ndi ana a m’bale wanga Benjamini?”+ Poyankha, Yehova anati: “Pita, kamenyane naye.”
23 Ndiyeno ana a Isiraeli anapita ku Beteli ndipo analira+ pamaso pa Yehova mpaka madzulo. Iwo anafunsira kwa Yehova, kuti: “Kodi ndipitenso kukamenyana ndi ana a m’bale wanga Benjamini?”+ Poyankha, Yehova anati: “Pita, kamenyane naye.”