Oweruza 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Isiraeli,+ moti anawapereka m’manja mwa ofunkha, ndipo anayamba kufunkha zinthu zawo.+ Iye anawagulitsa kwa adani awo owazungulira+ moti sanathe kuima pamaso pa adani awo.+ Yohane 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yesu anamuyankha kuti: “Simukanakhala ndi mphamvu iliyonse pa ine mukanapanda kupatsidwa kuchokera kumwamba.+ Ndiye chifukwa chake munthu amene wandipereka ine kwa inu ali ndi tchimo lalikulu kwambiri.”
14 Pamenepo mkwiyo wa Yehova unayakira Isiraeli,+ moti anawapereka m’manja mwa ofunkha, ndipo anayamba kufunkha zinthu zawo.+ Iye anawagulitsa kwa adani awo owazungulira+ moti sanathe kuima pamaso pa adani awo.+
11 Yesu anamuyankha kuti: “Simukanakhala ndi mphamvu iliyonse pa ine mukanapanda kupatsidwa kuchokera kumwamba.+ Ndiye chifukwa chake munthu amene wandipereka ine kwa inu ali ndi tchimo lalikulu kwambiri.”