-
1 Mbiri 28:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Komabe, m’nyumba yonse ya bambo anga+ Yehova Mulungu wa Isiraeli anasankha ineyo kuti ndikhale mfumu+ ya Isiraeli mpaka kalekale, popeza anasankha Yuda kuti akhale mtsogoleri.+ M’nyumba ya Yuda anasankhamo nyumba ya bambo anga.+ Pa ana a bambo anga+ anavomereza ineyo+ kuti ndikhale mfumu ya Isiraeli yense.
-