Oweruza 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo Baraki anasonkhanitsa pamodzi fuko la Zebuloni+ ndi fuko la Nafitali ku Kedesi, moti amuna 10,000 anam’tsatira,+ ndipo Debora nayenso anapita nawo. Oweruza 6:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Iye anatumiza mithenga+ m’dera lonse la fuko la Manase, ndipo anthu a m’fuko limeneli nawonso anasonkhana pamodzi n’kuyamba kumutsatira. Anatumizanso mithenga m’madera onse a mafuko a Aseri, Zebuloni ndi Nafitali, ndipo nawonso anabwera kudzakumana naye. 1 Mbiri 12:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 A fuko la Zebuloni,+ onse oyenerera kupita kunkhondo, kukafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo ndi zida zawo zonse zankhondo, analipo 50,000. Popita kwa Davide, iwo sanapite ndi mitima iwiri. Salimo 68:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pali fuko laling’ono la Benjamini limene likugonjetsa anthu,+Pali akalonga a Yuda pamodzi ndi makamu awo amene akufuula,Palinso akalonga a Zebuloni ndi akalonga a Nafitali.+
10 Ndipo Baraki anasonkhanitsa pamodzi fuko la Zebuloni+ ndi fuko la Nafitali ku Kedesi, moti amuna 10,000 anam’tsatira,+ ndipo Debora nayenso anapita nawo.
35 Iye anatumiza mithenga+ m’dera lonse la fuko la Manase, ndipo anthu a m’fuko limeneli nawonso anasonkhana pamodzi n’kuyamba kumutsatira. Anatumizanso mithenga m’madera onse a mafuko a Aseri, Zebuloni ndi Nafitali, ndipo nawonso anabwera kudzakumana naye.
33 A fuko la Zebuloni,+ onse oyenerera kupita kunkhondo, kukafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo ndi zida zawo zonse zankhondo, analipo 50,000. Popita kwa Davide, iwo sanapite ndi mitima iwiri.
27 Pali fuko laling’ono la Benjamini limene likugonjetsa anthu,+Pali akalonga a Yuda pamodzi ndi makamu awo amene akufuula,Palinso akalonga a Zebuloni ndi akalonga a Nafitali.+