Genesis 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kenako, Yakobo ananyamuka n’kupitiriza ulendo wake wopita Kum’mawa.+ Oweruza 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepa n’kuti Zeba ndi Zalimuna+ ali ku Karikori pamodzi ndi asilikali awo okwana pafupifupi 15,000. Asilikaliwa ndi amene anatsala pa gulu lonse la asilikali a Kum’mawa,+ ndipo amene anali ataphedwa anali asilikali 120,000.+ 1 Mafumu 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Nzeru za Solomo zinaposa+ nzeru za anthu onse a Kum’mawa+ ndi nzeru zonse za ku Iguputo.+
10 Pamenepa n’kuti Zeba ndi Zalimuna+ ali ku Karikori pamodzi ndi asilikali awo okwana pafupifupi 15,000. Asilikaliwa ndi amene anatsala pa gulu lonse la asilikali a Kum’mawa,+ ndipo amene anali ataphedwa anali asilikali 120,000.+