Oweruza 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepa n’kuti Zeba ndi Zalimuna+ ali ku Karikori pamodzi ndi asilikali awo okwana pafupifupi 15,000. Asilikaliwa ndi amene anatsala pa gulu lonse la asilikali a Kum’mawa,+ ndipo amene anali ataphedwa anali asilikali 120,000.+
10 Pamenepa n’kuti Zeba ndi Zalimuna+ ali ku Karikori pamodzi ndi asilikali awo okwana pafupifupi 15,000. Asilikaliwa ndi amene anatsala pa gulu lonse la asilikali a Kum’mawa,+ ndipo amene anali ataphedwa anali asilikali 120,000.+