11 Kenako, kunabwera mngelo wa Yehova+ ndi kukhala pansi pa mtengo waukulu umene unali ku Ofira. Mtengo umenewu unali wa Yowasi, Mwabi-ezeri.+ Pa nthawiyi, Gidiyoni+ mwana wa Yowasi, anali kupuntha tirigu moponderamo mphesa kuti akamubise mwamsanga Amidiyani asanaone.