1 Samueli 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Funsa anyamata ako zimenezi ndipo akuuza. Motero uwakomere mtima anyamata anga chifukwa tabwera tsiku labwino. Chonde, ugawire atumiki ako ndi mwana wako Davide chilichonse chimene dzanja lako lingapeze.’”+ 2 Samueli 17:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 anabweretsa makama, mabeseni, ziwiya zadothi, tirigu, balere, ufa,+ tirigu wokazinga,+ nyemba zikuluzikulu,+ mphodza+ ndi tirigu wowamba.
8 Funsa anyamata ako zimenezi ndipo akuuza. Motero uwakomere mtima anyamata anga chifukwa tabwera tsiku labwino. Chonde, ugawire atumiki ako ndi mwana wako Davide chilichonse chimene dzanja lako lingapeze.’”+
28 anabweretsa makama, mabeseni, ziwiya zadothi, tirigu, balere, ufa,+ tirigu wokazinga,+ nyemba zikuluzikulu,+ mphodza+ ndi tirigu wowamba.