Deuteronomo 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Ukakafika m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa, n’kulitengadi kukhala lako ndi kukhalamo,+ pamenepo iwe n’kunena kuti, ‘Ndidziikire mfumu ngati mitundu ina yonse yondizungulira,’+ Oweruza 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Kalekale mitengo inafuna kudzoza mfumu yawo. Pamenepo mitengoyo inauza mtengo wa maolivi+ kuti, ‘Iwe ukhale mfumu yathu.’+ 1 Samueli 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma zimenezi zinamuipira Samueli, chifukwa iwo anati: “Utipatse mfumu yoti izitiweruza.” Pamenepo Samueli anayamba kupemphera kwa Yehova.+ 1 Samueli 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mutaona kuti mfumu ya ana a Amoni, Nahasi,+ yabwera kudzamenyana nanu, munayamba kundiuza kuti, ‘Ife tikufuna kuti mfumu izitilamulira!’+ ngakhale kuti Yehova Mulungu wanu ndiye Mfumu yanu.+ Hoseya 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Tsopano mfumu yako ili kuti, kuti ikupulumutse m’mizinda yako yonse.+ Oweruza ako ali kuti amene unawauza kuti, ‘Ndipatseni mfumu ndi akalonga’?+
14 “Ukakafika m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa, n’kulitengadi kukhala lako ndi kukhalamo,+ pamenepo iwe n’kunena kuti, ‘Ndidziikire mfumu ngati mitundu ina yonse yondizungulira,’+
8 “Kalekale mitengo inafuna kudzoza mfumu yawo. Pamenepo mitengoyo inauza mtengo wa maolivi+ kuti, ‘Iwe ukhale mfumu yathu.’+
6 Koma zimenezi zinamuipira Samueli, chifukwa iwo anati: “Utipatse mfumu yoti izitiweruza.” Pamenepo Samueli anayamba kupemphera kwa Yehova.+
12 Mutaona kuti mfumu ya ana a Amoni, Nahasi,+ yabwera kudzamenyana nanu, munayamba kundiuza kuti, ‘Ife tikufuna kuti mfumu izitilamulira!’+ ngakhale kuti Yehova Mulungu wanu ndiye Mfumu yanu.+
10 “Tsopano mfumu yako ili kuti, kuti ikupulumutse m’mizinda yako yonse.+ Oweruza ako ali kuti amene unawauza kuti, ‘Ndipatseni mfumu ndi akalonga’?+