1 Samueli 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amuna onse amene anali kusautsidwa,+ onse amene anali ndi ngongole,+ ndi onse amene anali ndi zodandaula+ anayamba kusonkhana kwa iye,+ ndipo iye anakhala mtsogoleri wawo.+ Anthu onse amene anali naye anakwana 400.
2 Amuna onse amene anali kusautsidwa,+ onse amene anali ndi ngongole,+ ndi onse amene anali ndi zodandaula+ anayamba kusonkhana kwa iye,+ ndipo iye anakhala mtsogoleri wawo.+ Anthu onse amene anali naye anakwana 400.