2 Samueli 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamapeto pake, Abisalomu anauza atumiki ake kuti: “Pafupi ndi munda wanga pali munda wa Yowabu umene uli ndi balere. Mupite kumeneko ndipo mukautenthe ndi moto.”+ Choncho atumiki a Abisalomu anatentha mundawo ndi moto.+
30 Pamapeto pake, Abisalomu anauza atumiki ake kuti: “Pafupi ndi munda wanga pali munda wa Yowabu umene uli ndi balere. Mupite kumeneko ndipo mukautenthe ndi moto.”+ Choncho atumiki a Abisalomu anatentha mundawo ndi moto.+