Machitidwe 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma chiwembu chawocho chinadziwika kwa Saulo. Komabe iwo anali kuyang’anira mosamala m’zipata zonse usana ndi usiku kuti amuphe.+ 2 Akorinto 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ku Damasiko, bwanamkubwa wa mfumu Areta anali kulondera mzinda wa Adamasiko kuti andigwire,+
24 Koma chiwembu chawocho chinadziwika kwa Saulo. Komabe iwo anali kuyang’anira mosamala m’zipata zonse usana ndi usiku kuti amuphe.+