1 Samueli 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Atadzuka m’mawa kwambiri tsiku lotsatira, anapezanso kuti Dagoni wagwa pansi chafufumimba patsogolo pa likasa la Yehova. Anapeza mutu wa Dagoni ndi zikhatho zake zitaduka ndi kugwera pakhomo.+ Mbali yooneka ngati nsomba* ndi imene inatsala.
4 Atadzuka m’mawa kwambiri tsiku lotsatira, anapezanso kuti Dagoni wagwa pansi chafufumimba patsogolo pa likasa la Yehova. Anapeza mutu wa Dagoni ndi zikhatho zake zitaduka ndi kugwera pakhomo.+ Mbali yooneka ngati nsomba* ndi imene inatsala.