Oweruza 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno anayamba kuwakantha koopsa.* Kenako anayamba kukhala m’phanga la m’thanthwe la Etami.+ Oweruza 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamenepo Samisoni anati: “Ndi fupa la nsagwada za bulu wamphongo—milumilu! Ndi fupa la nsagwada za bulu wamphongo, ndapha anthu 1,000.”+
16 Pamenepo Samisoni anati: “Ndi fupa la nsagwada za bulu wamphongo—milumilu! Ndi fupa la nsagwada za bulu wamphongo, ndapha anthu 1,000.”+