Miyambo 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ngakhale pamene munthu akuseka, mtima wake ukhoza kukhala ukupweteka.+ Ndipo kusangalala kumathera m’chisoni.+ Mateyu 27:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Komanso analuka chisoti chachifumu chaminga ndi kumuveka kumutu n’kumupatsa bango m’dzanja lake lamanja. Kenako anamugwadira ndi kum’chitira zachipongwe+ kuti: “Mtendere ukhale nanu, inu Mfumu ya Ayuda!”+
13 Ngakhale pamene munthu akuseka, mtima wake ukhoza kukhala ukupweteka.+ Ndipo kusangalala kumathera m’chisoni.+
29 Komanso analuka chisoti chachifumu chaminga ndi kumuveka kumutu n’kumupatsa bango m’dzanja lake lamanja. Kenako anamugwadira ndi kum’chitira zachipongwe+ kuti: “Mtendere ukhale nanu, inu Mfumu ya Ayuda!”+