Salimo 74:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kumbukirani izi: Inu Yehova, mdani wakuchitirani mopanda ulemu,+Ndipo anthu opusa anyoza dzina lanu.+ Yeremiya 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu Yehova mukudziwa bwino mavuto anga.+ Ndikumbukireni+ ndipo mutembenuke ndi kundiyang’ana kuti mubwezere anthu ondizunza.+ Musandichotsere moyo wanga chifukwa chakuti simupsa mtima mwamsanga.+ Onani chitonzo chimene chili pa ine chifukwa cha dzina lanu.+
18 Kumbukirani izi: Inu Yehova, mdani wakuchitirani mopanda ulemu,+Ndipo anthu opusa anyoza dzina lanu.+
15 Inu Yehova mukudziwa bwino mavuto anga.+ Ndikumbukireni+ ndipo mutembenuke ndi kundiyang’ana kuti mubwezere anthu ondizunza.+ Musandichotsere moyo wanga chifukwa chakuti simupsa mtima mwamsanga.+ Onani chitonzo chimene chili pa ine chifukwa cha dzina lanu.+