Genesis 47:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chotero Yosefe anakhazika bambo ake ndi abale akewo ku Iguputo. Anawapatsa malo abwino koposa a dzikolo ku Ramese,+ monga mmene Farao analamulira. Ekisodo 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako+ kuti masiku ako atalike m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+ Miyambo 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Bambo wa munthu wolungama ndithu adzasangalala.+ Bambo wobereka mwana wanzeru adzakondwera naye.+ Mateyu 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako,+ komanso lakuti, Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.”+
11 Chotero Yosefe anakhazika bambo ake ndi abale akewo ku Iguputo. Anawapatsa malo abwino koposa a dzikolo ku Ramese,+ monga mmene Farao analamulira.
12 “Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako+ kuti masiku ako atalike m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.+