Rute 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Obedi anabereka Jese,+ ndipo Jese anabereka Davide.+ 1 Samueli 20:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tsiku lotsatizana ndi tsiku lokhala mwezi, tsiku lachiwiri, mpando wa Davide unakhalabe wopanda munthu. Choncho Sauli anafunsa mwana wake Yonatani kuti: “N’chifukwa chiyani mwana wa Jese+ sanabwere ku chakudya dzulo ndi lero?” 1 Samueli 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo Nabala anayankha atumiki a Davide kuti: “Kodi Davide ndani,+ ndipo mwana wa Jese ndani? Masiku ano atumiki amene akuthawa ambuye awo achuluka kwabasi.+
27 Tsiku lotsatizana ndi tsiku lokhala mwezi, tsiku lachiwiri, mpando wa Davide unakhalabe wopanda munthu. Choncho Sauli anafunsa mwana wake Yonatani kuti: “N’chifukwa chiyani mwana wa Jese+ sanabwere ku chakudya dzulo ndi lero?”
10 Pamenepo Nabala anayankha atumiki a Davide kuti: “Kodi Davide ndani,+ ndipo mwana wa Jese ndani? Masiku ano atumiki amene akuthawa ambuye awo achuluka kwabasi.+