1 Samueli 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yonatani ndi Davide anachita pangano,+ chifukwa Yonatani anali kukonda Davide ngati mmene anali kudzikondera.+ 1 Samueli 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho Yonatani analumbiranso kwa Davide chifukwa chakuti anali kum’konda kwambiri. Pakuti Yonatani anali kukonda Davide monga mmene anali kudzikondera iye mwini.+
3 Yonatani ndi Davide anachita pangano,+ chifukwa Yonatani anali kukonda Davide ngati mmene anali kudzikondera.+
17 Choncho Yonatani analumbiranso kwa Davide chifukwa chakuti anali kum’konda kwambiri. Pakuti Yonatani anali kukonda Davide monga mmene anali kudzikondera iye mwini.+