1 Samueli 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako Davide anafika ku Nobu+ kwa Ahimeleki wansembe. Ahimeleki+ ataona Davide anayamba kunjenjemera, ndipo anam’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani uli wekha popanda munthu wina?”+
21 Kenako Davide anafika ku Nobu+ kwa Ahimeleki wansembe. Ahimeleki+ ataona Davide anayamba kunjenjemera, ndipo anam’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani uli wekha popanda munthu wina?”+