-
Oweruza 5:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 ‘Kodi sanapeze zofunkha ndipo ayenera kuzigawa?+
Kodi sayenera kugawa mkazi mmodzi, kapenanso akazi awiri kwa mwamuna aliyense wamphamvu,+
Ndi nsalu za Sisera zofunkhidwa zonyika mu utoto, ndithu nsalu zofunkhidwa zonyika mu utoto?
Kodi sayenera kugawa chovala chopeta chonyika mu utoto, inde, zovala ziwiri zopeta,
Kuti amuna ofunkha avale m’makosi awo?’
-