Oweruza 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Iye anawauzadi mmene angalowere mumzindawo, ndipo iwo anapha anthu a mumzindawo ndi lupanga,+ koma anasiya mwamunayo ndi banja lake lonse ali amoyo.+
25 Iye anawauzadi mmene angalowere mumzindawo, ndipo iwo anapha anthu a mumzindawo ndi lupanga,+ koma anasiya mwamunayo ndi banja lake lonse ali amoyo.+