1 Samueli 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Elikana anapita kunyumba kwake ku Rama, koma mwanayo anakhala mtumiki+ wa Yehova pamaso pa wansembe Eli. 1 Samueli 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Samueli anali kutumikira+ pamaso pa Yehova, ali mwana ndipo anali kuvala efodi wansalu.+
11 Kenako Elikana anapita kunyumba kwake ku Rama, koma mwanayo anakhala mtumiki+ wa Yehova pamaso pa wansembe Eli.