Genesis 33:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Esau anati: “Chabwino, ndiye ndikupatseko ena mwa anyamata angawa kuti akuthandize.” Koma iye anati: “Ayi musachite kutero. Musavutike mbuyanga,+ ndiyenda bwinobwino.” Rute 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atamva zimenezi Rute anati: “Mwandikomera mtima mbuyanga. Mwanditonthoza mtima, komanso mwalankhula mondilimbitsa mtima+ ngati kuti ndine mtsikana wanu wantchito pamene sindili mmodzi wa atsikana anu antchito.”+
15 Ndiyeno Esau anati: “Chabwino, ndiye ndikupatseko ena mwa anyamata angawa kuti akuthandize.” Koma iye anati: “Ayi musachite kutero. Musavutike mbuyanga,+ ndiyenda bwinobwino.”
13 Atamva zimenezi Rute anati: “Mwandikomera mtima mbuyanga. Mwanditonthoza mtima, komanso mwalankhula mondilimbitsa mtima+ ngati kuti ndine mtsikana wanu wantchito pamene sindili mmodzi wa atsikana anu antchito.”+