1 Samueli 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo Hana anayankha kuti: “Ayi mbuyanga! Ine ndine mkazi wopsinjika maganizo. Sindinamwe vinyo kapena chakumwa choledzeretsa ayi, koma ndikufotokoza nkhawa zanga zonse kwa Yehova.+
15 Pamenepo Hana anayankha kuti: “Ayi mbuyanga! Ine ndine mkazi wopsinjika maganizo. Sindinamwe vinyo kapena chakumwa choledzeretsa ayi, koma ndikufotokoza nkhawa zanga zonse kwa Yehova.+