1 Samueli 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu olanda katundu anali kutuluka mumsasa wa Afilisiti m’magulu atatu.+ Gulu loyamba linali kulowera kumsewu wopita ku Ofira,+ kudera la Suwali.
17 Anthu olanda katundu anali kutuluka mumsasa wa Afilisiti m’magulu atatu.+ Gulu loyamba linali kulowera kumsewu wopita ku Ofira,+ kudera la Suwali.