Ekisodo 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Yehova anauza Mose kuti: “Lemba zimenezi m’buku monga chikumbutso+ ndi kumuuza Yoswa kuti, ‘M’kupita kwa nthawi ndidzafafaniziratu Aamaleki padziko lapansi* ndipo sadzakumbukika n’komwe.’”+ Deuteronomo 25:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Motero Yehova Mulungu wanu akakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti mulitenge kukhala cholowa chanu,+ mufafanize dzina la Amaleki pansi pa thambo.+ Musaiwale zimenezi. 1 Mbiri 4:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Iwo anapha Aamaleki+ otsala omwe anathawa, ndipo akukhala kumeneko mpaka lero.
14 Tsopano Yehova anauza Mose kuti: “Lemba zimenezi m’buku monga chikumbutso+ ndi kumuuza Yoswa kuti, ‘M’kupita kwa nthawi ndidzafafaniziratu Aamaleki padziko lapansi* ndipo sadzakumbukika n’komwe.’”+
19 Motero Yehova Mulungu wanu akakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti mulitenge kukhala cholowa chanu,+ mufafanize dzina la Amaleki pansi pa thambo.+ Musaiwale zimenezi.