1 Samueli 15:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Samueli analirira+ Sauli ndipo sanaonanenso naye mpaka tsiku la imfa yake. Koma Yehova anamva chisoni kuti anaika Sauli kukhala mfumu ya Isiraeli.+ Mlaliki 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nthawi yolira+ ndi nthawi yoseka.+ Nthawi yolira mofuula+ ndi nthawi yodumphadumpha mosangalala.+
35 Samueli analirira+ Sauli ndipo sanaonanenso naye mpaka tsiku la imfa yake. Koma Yehova anamva chisoni kuti anaika Sauli kukhala mfumu ya Isiraeli.+