2 Samueli 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Davide anatumizanso mithenga kwa Isi-boseti+ mwana wa Sauli ndi uthenga wonena kuti: “Ndipatse mkazi wanga Mikala, amene ndinalonjeza kumukwatira mwa kupereka makungu 100 akunsonga+ a Afilisiti.”
14 Davide anatumizanso mithenga kwa Isi-boseti+ mwana wa Sauli ndi uthenga wonena kuti: “Ndipatse mkazi wanga Mikala, amene ndinalonjeza kumukwatira mwa kupereka makungu 100 akunsonga+ a Afilisiti.”