11 Ndiyeno Mfumu Davide inatumiza uthenga kwa Zadoki+ ndi Abiyatara+ ansembe kuti: “Lankhulani ndi akulu a Yuda+ kuti, ‘N’chifukwa chiyani inu nokha simukuchitapo kanthu kuti mfumu ibwerere kunyumba yake, pamene Aisiraeli onse atumiza uthenga kwa mfumu kumene ikukhala?