Salimo 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ali kumwamba, Yehova anayamba kugunda ngati mabingu,+Wam’mwambamwamba anayamba kutulutsa mawu ake,+Anatulutsanso matalala ndi makala onyeka a moto. Yesaya 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yehova adzapangitsa kuti ulemerero wa mawu ake+ umveke. Adzapangitsa kuti dzanja lake limene likutsika lionekere.+ Dzanjalo lidzatsika ndi mkwiyo waukulu,+ lawi la moto wowononga,+ mvula yamphamvu ndiponso yamkuntho+ ndi matalala.+
13 Ali kumwamba, Yehova anayamba kugunda ngati mabingu,+Wam’mwambamwamba anayamba kutulutsa mawu ake,+Anatulutsanso matalala ndi makala onyeka a moto.
30 Yehova adzapangitsa kuti ulemerero wa mawu ake+ umveke. Adzapangitsa kuti dzanja lake limene likutsika lionekere.+ Dzanjalo lidzatsika ndi mkwiyo waukulu,+ lawi la moto wowononga,+ mvula yamphamvu ndiponso yamkuntho+ ndi matalala.+