1 Mbiri 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mtsogoleri wa 9, wa mwezi wa 9, anali Abi-ezeri+ Muanatoti,+ wochokera mwa Abenjamini. Gulu lake linali ndi anthu 24,000.
12 Mtsogoleri wa 9, wa mwezi wa 9, anali Abi-ezeri+ Muanatoti,+ wochokera mwa Abenjamini. Gulu lake linali ndi anthu 24,000.