2 Samueli 3:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Anthu onse anaona zimene zachitika, ndipo anaona kuti zimene mfumu ikuchita zili bwino. Mofanana ndi zonse zimene mfumuyo inachita, anthu onse anaona kuti izinso zili bwino.+ Aheberi 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso, musaiwale kuchita zabwino+ ndi kugawana zinthu ndi ena, pakuti nsembe zotero Mulungu amakondwera nazo.+
36 Anthu onse anaona zimene zachitika, ndipo anaona kuti zimene mfumu ikuchita zili bwino. Mofanana ndi zonse zimene mfumuyo inachita, anthu onse anaona kuti izinso zili bwino.+
16 Komanso, musaiwale kuchita zabwino+ ndi kugawana zinthu ndi ena, pakuti nsembe zotero Mulungu amakondwera nazo.+